Malawi Seventh-Day Adventist Music

Malawi Seventh-Day Adventist Music To advertise and promote about malawian good gospel music to the world
(2)

11/06/2026

Agulu mwafika kale kolimbikira? osaonesa ntima onyanyala Mulungu apatsa olimbikira..

Good morning Agulu lero kwachera Birthday ya Pastor Davie Chiwaya  HAPPY BIRTHDAY Timakunyadilani...
11/06/2026

Good morning Agulu lero kwachera Birthday ya Pastor Davie Chiwaya
HAPPY BIRTHDAY Timakunyadilani...

10/06/2026

Agulu tsiku latha bwanji kumeneko? Taonelani kanyimbo kabwino koimbidwa ndi Ephesians Music Ministry

Agulu ku tiyeni kwa Saturday  kwapezeka, save the date.
10/06/2026

Agulu ku tiyeni kwa Saturday kwapezeka, save the date.

10/06/2026

Good morning Agulu, kwacha bwanji kumeneko?

09/06/2026

Agulu mbiri inalembedwa ku Dukathole S.D.A Church kuti Namasalima Singer's inawayendera last year ndipo ife a Media tinasunga nkhani ndiyoti ndithu azatankha...

09/06/2026

Agulu tsiku latha bwanji konse komwe muli?

08/06/2026

Agulu tiyeni tilimbikile heaven is waiting, Mixed Voices Reunion inayimba kale ndipo zizindikiro zukwanila.

Agulu ndi nyimbo iti ya Mama Florence Massea music ministry.  Yomwe imakusangalatsani inuyo?Mukafuna kulengeza zochitila...
08/06/2026

Agulu ndi nyimbo iti ya Mama Florence Massea music ministry. Yomwe imakusangalatsani inuyo?
Mukafuna kulengeza zochitila olo kumva zambiri contact us on WhatsApp +265992800187

08/06/2026

Agulu meet Mapingo FAm
Kuombatu kuimbatu, link in comment section..

Address

Seventh-Day Adventist Church
Germiston

Telephone

+265992800187

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Malawi Seventh-Day Adventist Music posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share