17/01/2025
Mellz Kumpanje πͺπ₯
Chomwe ndimaziwa ine ndi chakuti "Munthu sumacheza wekha"...akulu akulu, uyu ndili naye pa chithunziyu ndi Bandera music ...ndipo ndikukhulupilira kuti tonse Pano nkhani yake tikuidziwa...ndikunena Pano,adakali mmanja mwa a police akumusunga mchitokosi...fast fast forward, munthuyi akukanika kutuluka kunali kuja chifukwa alibe lawyer omuthandizila kuti nkhani ikambidwe imalizidwe kuti atulukeko...nde ine ndili ndi mzanga lawyer amenenso ndi DJ, ndayesa kukamba naye... kutengera ndi mmene ama chargila ma lawyer komanso poti ndiwaku Blantyre,Kwa ineyo ndikuona kuti ndi fair price kutengela ndi mtengowo, koma mwandekha ngati munthu sindingakwanise...wanena kuti timupase MK650,000 mmalo mwa 1,000,000 pakuti Bandera ndi munthu oti tonse Tili mu field imodzi...koma pamwamba pa 650 timuikilepo MK500,000 yamafuta yoyendera 3 hearings...imene tikawerengera ikukwana MK1,150,000....nde ndimati ndikupempheni mundithandize limodzi limodzi kuti ndalamayi ikwane timutuluseko m'bale wathu uja ngati kuthekela kutelo muli nako...any amount will appreciated....Ayao amzanga tiliko Mesa??....
You can send through these accounts :
Airtel money : 0995072049 (Mellanie Joseph Msumba
Mpamba : 0885531911 (Kevin Chidothi)
National Bank : 1008151818
Ma transaction onse ndizaika pa page p***a muzaone...
Zikomo Mulungu akudalitseniπ