Gìst Malawi

Gìst Malawi Gist Malawi provide the Best of Malawian and African content , entertainment,Music ,news,fashion, Lifestyle,comedy relationships and lots more.��

06/04/2026

Chilichonse chochitika pasi pa dambo
Zaulura.😈

Apwetekana!!!

02/04/2026

BENGO KU DZIKO LA CHILENDO.

Bengo Maluzi Atamumenya Anaganiza Zopita Kunja Kukasaka Ntchito Monga Anthu Amachitila Kupita Theba,koma Iyeyo Anapita Ku Nigeria.Atafika Mwamwayi Ntchito Anayipeza Koma Ya House Boy.

Anapatsidwa Malamulo Monga Mukudziwa Pa Ntchito Iriyonse Pamakhala Malamulo.Koma Panali Lamulo Limodzi Lomwe Bengo Linamudabwitsa Loti Osalowa Kuchipindga Ichi.

Bengo Anavomera Kulemekeza Malamulo Antchito Yake Ndipo Samalowadi Kuchipinda Chija.Koma Chomwe Chimamudabwitsa Ndi Choti Bwana Ake Akabwera Madzulo Amatenga Mbale Ya Za Kudya Ndi Madzi Kukasiya Kuchipinda Kuja,izi Zimachitika Madzulo A tsiku Lirilonse.

Bengo Anali Ndi Mafuso Mmutu Mwake Koma Opanda Mayankho,paja Ndinabwerera Kuno Ncthito Ndizingopanga Zomwe Ndina Bwerera Kuno.Kunyumba Kuja Kumabwera Anthu Ambiri Kudzacheza Ndi Abwana A Bengo Ndipo Amawayamikila K*t Ali Ndi Mnyamata Wa Bwino Olimbikila.Eya Ndiwokhulupilika Anatero Abwana.

Tsiku Lina Bengo Akukolopa Anapeza Ma Key Ndipo Sanakayikile K*t Ndi Akuchipinda Choletsedwa.

Dikilani part 2 Osaiwala kupanga follow and share Gìst Malawi isakuponyeni

02/04/2026

Ndi Booza liti Munalivelako Pa Bakili muluzi TV🙌🫵

21/11/2025

Bola Pamenepa Bail patiiii✊ spirituality of life.

16/09/2025

Kwacha Bwanji

Tiyeni tivote mwa Nzeru lero🗳

Address

Lilongwe

Opening Hours

Monday 08:00 - 17:00

Telephone

+265990549290

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Gìst Malawi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Gìst Malawi:

Share