DJ Mad Gee

DJ Mad Gee Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from DJ Mad Gee, DJ, Kasungu.

04/11/2022

Say no to ❌suicideπŸš«πŸ™πŸ™

Happy birthday duntu Che Kalonda 😎
03/11/2022

Happy birthday duntu

Che Kalonda 😎

02/11/2022

DJ mad gee is back😎😎😎

Be Transparent And Stop Lying To Your Partners  ( Gibwa De Artist  )" Masiku ano, amuna ambiri akunamiza akazi kuti amaw...
02/11/2022

Be Transparent And Stop Lying To Your Partners ( Gibwa De Artist )

" Masiku ano, amuna ambiri akunamiza akazi kuti amawakonda kuti angowadya nkuwataya.

Komanso akazi alero ambiri amanamiza amuna andalama kuti amawakonda cholinga awadyele ndalama nkuwataya.

Mapeto ake ndi depression.

I believe that many heartbreaks that lead to depression are because of lies.

Ma guy, ngati mkaziyo sumamufila usamunamize zoti umamukonda chifukwa amayamba kukukhulupilila kenako akazaziwa kuti umangofuna udye amasweka mtima and end result ndi depression.

Akazi nso nawo asiye kunamiza amuna kuti amawakonda koma akungofuna ndalama zawo, ndalamazo zikatha nkuwasiya.

Izi zimathela depression.

Tatiyeni tikhale anthu achilungamo chonde. Bodza ndilimene likutivulaza anthufe.

This is something I wrote some time back when I got heartbroken "- Musician, Gibwa says the best way to reduce issues of depression caused by heartbreaks is for partners in a relationship to be transparent and honest with each other.

Full video https://youtu.be/Ni1ctHPEvJc

Copied Mikozi

Gibwa _Bwenzi (Official 4K Music Video) [dir by Mzati Msash]

Address

Kasungu

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when DJ Mad Gee posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category