BLUE TICK SOUNDs

BLUE TICK SOUNDs This group is about sound systems to help people to find easy dj and good quality sound systems.

24/11/2025

Amuna opanda ndalama sikunyekhula kwake kuchipinda πŸ˜©πŸ™Œ

23/11/2025

koma guys ndalama zikuwononga anthu maka asikanawa osafuna kungwira ntchito...

22/11/2025

album yose nyimbo yabwino ndiyomwe waimba ndi Minad.
wachedwa

pali nyimbo yomwe ikufuna kutulusidwa ndi zegede and nyimboyi ndiya ife a blueticksounds... and tinalipa ngwirizano oti ...
19/11/2025

pali nyimbo yomwe ikufuna kutulusidwa ndi zegede and nyimboyi ndiya ife a blueticksounds... and tinalipa ngwirizano oti tingwire nawo abiti naje nkhani za maimbidwe tinatulusa nyimbo yathu yoyamba pa ngwirizano wathu "BWEZI UKUNYOZA" itatuluka panali mavuto ena ndi zegede not abiti naje ayi zomwe zinapangisa kuimisa project management yathu and tili odabwa kuwona kt nyimbo zomwe timapanga ife zakaimbidwa kwina... mu nyimbo ya abiti naje muwonamo log ya blueticksounds and fire fly... and log ya voice oops... Mikozi ndaona pa page yanu chonde izi zisachitike chifukwa nyimbo ndiyobedwa .... thanks... Blueticksounds management.

pali nyimbo yomwe ikufuna kutulusidwa ndi zegede and nyimboyi ndiya ife a blueticksounds... and tinalipa ngwirizano oti ...
19/11/2025

pali nyimbo yomwe ikufuna kutulusidwa ndi zegede and nyimboyi ndiya ife a blueticksounds... and tinalipa ngwirizano oti tingwire nawo abiti naje nkhani za maimbidwe tinatulusa nyimbo yathu yoyamba pa ngwirizano wathu "BWEZI UKUNYOZA" itatuluka panali mavuto ena ndi zegede not abiti naje ayi zomwe zinapangisa kuimisa project management yathu and tili odabwa kuwona kt nyimbo zomwe timapanga ife zakaimbidwa kwina... mu nyimbo ya abiti naje muwonamo log ya blueticksounds and fire fly... and log ya voice oops... Mikozi chonde izi zisachitike chifukwa nyimbo ndiyobedwa .... thanks... Blueticksounds management.

Ndipaseni 98 thousands yonga ndiliku Blantyre...
21/08/2025

Ndipaseni 98 thousands yonga ndiliku Blantyre...

Nduganiza zogawa chimwemwe changa kwama friends
16/08/2025

Nduganiza zogawa chimwemwe changa kwama friends

15/08/2025

cape town ☺️

Blueticksounds
06/08/2025

Blueticksounds

359 Followers, 423 Following, 265 Likes - Watch awesome short videos created by [email protected]

06/08/2025

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Precious En Dee, Lad Jay πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯ ivani kukoma

Address

MACHINJIRI
Blantyre

Telephone

+27611535057

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when BLUE TICK SOUNDs posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to BLUE TICK SOUNDs:

Share