CLIF NJOLO MR M.C

CLIF NJOLO MR M.C If you need your wedding ceremony to be successful, adorable & Presentable in all angles just consult

02/03/2026

I welcome you all my new followers and fill free if you have any question, If you have any suggestions which are contributory to this sector, it will be taken to consideration 🙏. You are my family on my on I can be nothing so take it in your heart that am so proud of you all🙏😃💪🤝.
Don't forget to consult us in all ur functions and we will be there for you.
MOTTO KUTI BUUUUU!!!!😃♥️🔥💥💯
Nkhuku zidyedwe Chaka Chino!!!!!!

07/01/2026

Pajatu zabwino salozelana 👉ndipo ikakhala njuchi🐝 umaloza iyo yakuluma. Tangowaitani Mr MC Njollo Clif ndipo simudzakhumudwa ndipo ma numbers ndi omwe Ali Mwambawo👆😃🙏💪🤝🎇🔥❤️💯

23/11/2025

Ndatitu kukumakhala ntchito, tangowayimbilani Mr MC Njollo pa +265 992 36 56 78 or email ku [email protected] kuti zabwinozi zisakuphonyeni pajatu kugona pakati nkuyambilira nanga muchedweranji😃🔥💪💯❤️🎇

Ndilero tiyeni tikayipatse Moto🔥 kwinaku mukuona kuti Kodi Mr MC Njollo amathadi?💪💯🎇. Wishing them all the best as they ...
01/11/2025

Ndilero tiyeni tikayipatse Moto🔥 kwinaku mukuona kuti Kodi Mr MC Njollo amathadi?💪💯🎇. Wishing them all the best as they are starting a new life🔥

Ndatitu mukamachedwa mukuchedwa nokha kuwaitana MR MC Njollo kumwambo wanuwo koma anzanu akulowa m'banja pa 1 Nov 2025 p...
14/10/2025

Ndatitu mukamachedwa mukuchedwa nokha kuwaitana MR MC Njollo kumwambo wanuwo koma anzanu akulowa m'banja pa 1 Nov 2025 pano tiyeni tikakumane kumeneko ndipo MR MC Njollo akakutsangalatsani kumeneku

Yesterday was so precious to me & all our family for we had a privilege to testify the wedding ceremony of my young bro ...
12/10/2025

Yesterday was so precious to me & all our family for we had a privilege to testify the wedding ceremony of my young bro Sam. Mmmm mwatichotsa manyazi achimwene & God be with ur family nakudalitseni mudela lirilonse lamoyo wanu wam'banja & kukhala pabanja sizophweka, sizabwino zokhazokha mabvutonso alimom'mo koma chachikulu kaphuzileni kulolelana, kumvetsetsana pakabvuta ndikupeza njira yothanirana ndibvutolo, ankhoswe siyankho lanu koma yankho lanu ndiye kumuopa Mulungu ndikumutenga iye akhale nkhoswe ya banja lanu mukatelo banja lanu lidzakha lolimba or Namondwe atabwera motani simudzagwedezeka🙏🤝❤️😃

Ngati mukufuna ukwati wanu ukometsetse or mwina muli ndi engagement and Cooperate functions etc just consult MC clif NJO...
12/09/2025

Ngati mukufuna ukwati wanu ukometsetse or mwina muli ndi engagement and Cooperate functions etc just consult MC clif NJOLLO .. MngoniWachiLhomwe mukatelo ndiye kuti zanu zatheka ndipo simudzakhumudwa konse. Kuli konse timafika🙏😄🔥

06/09/2025

Ndikati lero kunabvuta muzimvetsa just call us on +265 992 36 56 78 bac simudzakhumudwa😄💪

06/09/2025

Thus Clif Njolo the M.C on duty. If you are in need of our services please contact us on +265 992 36 56 78 bac mwatipeza. Izi za lero izi inu ukwati uzikoma osati mwapita kukwati bac kumabwerako mukulira ngati munali kumaliro😄💪🙆

Address

Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when CLIF NJOLO MR M.C posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category