11/06/2025
Thanks John Cloud 🔥🔥
Yanga yokonda kuonela nyimbo za ma upcoming artist amzanga ndaonelanso Stool sesssion ya artist wamkazi uyu dzina lake JEARLINE sindikuziwa kuti amakhala kuti koma chomwe ndinganene ndichoti ali ndi luso lachita kubadwa nalo losakakamiza
Keep going girl you are a star!!!!